Tilire maliro,
Munthu wamkulu watisiya,
Tigwetse msozi,
Popeza imfa yachita kaduka.
Tiyeni tilire
Tiyeni tionetse chisoni
Ngakhale ambiri sitimakondwa
Tiyenibe tilire maliro
Tiyeni tilire maliro
Lero ndife anamfedwa
Poti latisiya tokha kholo
Tiyeni tilire
No comments:
Post a Comment